Sitolo m’madera ambiri makamaka m’mizinda ikuluikulu zakhala zotseka mkati mwa sabatayi pomwe eni sitolozo sakugwirizana ndi njira yatsopano yotolera misonkho ya VAT yomwe nthambi ya misonkho ya MRA idakhazikitsa. Koma Lachinayi, ochita bizinesiwa adalengeza kuti ayambanso kuchita malonda awo. Kuyambira pa 1 May 2026, MRA idayamba kugwiritsa ntchito njira yotchedwa Electronic Invoicing System (EIS) yomwe … The post Njira yatsopano yotololera misonkho yautsa mapiri pa chigwa appeared first on Nation Online .