This article was originally published on Malawi24 ">Malawi24 , Malawi's #1 independent news platform. Kutakhala kupsa ndekuti kukhala kwa chigumu, pamwamba moto, pansi moto:; pena nkumafusa kuti kodi mayikowa achita kugwirizana kuti a Malawi tiwakhaulitse asamatuluke kunja? Posachedwapa, dziko la America lalengeza kuti lichotsa ofesi zopangira zilolezo zopitira mdzikolo m’mayiko ena kuphatikizapo Malawi zomwe zichititse kuti a Malawi ochuluka adzilephera kupitako.