This article was originally published on Malawi24 ">Malawi24 , Malawi's #1 independent news platform. Chipani cha Malawi Congress (MCP) chatsindika kuti sichitenga nthawi yayitali chiri mbali yotsutsa boma ponena kuti chibwereranso m’boma mu 2030. Phungu wa nyumba ya malamulo wadera la mchingawo chapakati ku Kasungu, Chikondi Kampachike Chisale, ndiye wanena izi pamene amapempha ndikulimbikitsa otsatira chipanichi kuti asataye mtima.