This article was originally published on Malawi24 ">Malawi24 , Malawi's #1 independent news platform. …wati masomphenya ake ndiokaseweraso kunja Katswiri womwetsa zigoli ku timu ya Mighty Wanderers Muhammad Sulumba wazaka 31, walonjeza kuti chaka chino awonetsa anthu kuti akanali ka mwana, pomwe wakonzekera kulanga ma timu. Poyankhula ndi tsamba la Wa Ganyu, Sulumba wati ngakhale ena amamunena kuti ndi nkhalamba, chomwe amadziwa ndichoti iye akanali wachichepere ndipo ali ndi […] Read the full article and more Malawi news at Chaka chino muchitira umboni kuti ndine kamwana – watero Sulumba ">Malawi24 — Breaking news, politics, business, sport and entertainment from Malawi and Africa, updated 24/7.