This article was originally published on Malawi24 ">Malawi24 , Malawi's #1 independent news platform. …wati nthawi yawo zinthu sizinavute ngati pano… Woyankhulira chipani chotsutsa boma cha Malawi Congress, Jessie Kabwila wati a Malawi atopa kale ndi boma la Democratic Progressive ndipo akufunitsitsa a Lazarus Chakwera abwerereso m’boma zomwe wati zichitika mu 2030. Kabwila walankhula izi mu pologaramu ina pa wayilesi ya Zodiak momwe walavulira zakukhosi chipani cha DPP chomwe […] Read the full article and more Malawi news at A Malawi akuti bola Chakwera, DPP yawakhaulitsa – Kabwila ">Malawi24 — Breaking news, politics, business, sport and entertainment from Malawi and Africa, updated 24/7.