Amene ajatu musamangowaona, palibe chilipo! Unamumva mmene Scott amadzitamilirira kuti ndi katsiwiri kuchipinda, iii, mhu, amwali zero pa teni. Kodi unamva kuti mwamuna was Estelle uja akutitu samamugwira olo.