This article was originally published on Malawi24 ">Malawi24 , Malawi's #1 independent news platform. “Chonde abambo ngati pali vuto tiyeni tivomereze, apo bii titha ndithu.” Awa ndi ena mwa malangizo omwe avumbwa m’masamba amchezo pomwe chiwerengero cha abambo omwe atsamaya alimkati mwa nkhondo chikumka chikwera. Chatsitsa dzaye nchoti White Sani, bambo wazaka 48 wochokera m’boma la Zomba, wafa sabata ino ku malo ogona alendo a Ketekete munzinda wa Blantyre […] Read the full article and more Malawi news at Pansi mtedza abambo: Imfa pambuyo panu ku maloji ">Malawi24 — Breaking news, politics, business, sport and entertainment from Malawi and Africa, updated 24/7.