This article was originally published on Malawi24 ">Malawi24 , Malawi's #1 independent news platform. Mphunzitsi wa time ya Ekhaya, Enos Chatama wati palibepo chifukwa choyankhulira kwambiri chifukwa cholepherana ndi FCB Nyasa Big Bullets. Poyankhula atatha masewero omwe Ekhaya FC inachokera kumbuyo ndikulepherana ndi Bullets pogoletsana chigoli chimodzi kwa chimodzi mu gawo loyamba la mpikisano wa Airtel Top 8, Chatama anati timu yake inali yaying’ono kwa Bullets ngakhale yakwanitsa kufananitsa […] Read the full article and more Malawi news at Kulepherana sindiye kuti takula kuposa BB -Chatama ">Malawi24 — Breaking news, politics, business, sport and entertainment from Malawi and Africa, updated 24/7.