Amalawi akudandaula usiku ndi usana kaamba ka kuthimathima kwa magetsi komwe akuti kwasokoneza mabizinesi ndi mabajeti m’mabanja chifukwa ena akuopa kuguliratu zinthu zofunika kusunga m’mafiriji. Tamvani atazungulira m’madera ena mu mzinda wa Lilongwe monga Shire ku Area 49 ndi Nsungwi Lachiwiri adapeza kuti magetsi adali othima ndipo ochita bizinesi zolira magetsi ena adali khale. A … The post Amalawi akulira ndi vuto la magetsi appeared first on Nation Online .